Genesis 41:33 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano inu mfumu sankhulani munthu wodziŵa zinthu ndi wanzeru, mumpatse ulamuliro pa dziko lonse la Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsopano, Farao afunefune munthu wakuzindikira ndi wanzeru, amkhazike iye ayang'anire dziko la Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsopano Farao apezeretu munthu wozindikira ndi wanzeru ndipo amuyike kukhala woyangʼanira dziko lonse la Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsopano, Farao afunefune'munthu wakuzindikira ndi wanzeru, amkhazike iye ayang'anire dziko la Aigupto.