Genesis 41:38 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Farao adafunsa nduna zakezo kuti, “Kodi tingampeze kuti munthu wina woposa uyu amene ali ndi mzimu wa Mulungu?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Farao anati kwa anyamata ake, Kodi ife tidzaone munthu ngati uyu, mzimu wa Mulungu uli m'mtima mwake?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Farao anafunsa nduna zake nati, “Kodi tingathe kumupeza munthu wina ngati uyu, amene ali ndi mzimu wa Mulungu?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Farao anati kwa anyamata ace, Kodi ife tidzaone munthu ngati uyu, mzimu wa Mulungu uli m'mtima mwace?