Genesis 41:40 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwe ndiwe amene udzalamulira dziko langa, ndipo anthu anga onse adzakumvera. Ine ndidzakupambana pa chokhachi choti ndine mfumu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Uziyang'anira pa nyumba yanga, ndipo anthu anga onse adzalamulidwa mwa mau ako; pa mpando wachifumu pokha ine ndidzakuposa iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwe ukhala nduna yayikulu mu dziko langa ndipo anthu onse adzamvera zimene walamula. Ine ndekha ndiye amene ndidzakuposa mphamvu chifukwa ndimakhala pa mpando waufumu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Uziyang'anira pa nyumba yanga, ndipo anthu anga onse adzalamulidwa mwa mau ako; pa mpando wacifumu pokha ine ndidzakuposa iwe.