Genesis 41:47 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa zaka zija za dzinthu dzambiri, m'dziko lonse munali chakudya chochuluka kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zaka zisanu ndi ziwiri zakuchuluka dzinthu nthaka inabala zambirimbiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mʼzaka zisanu ndi ziwiri za zokolola zambiri zija, anthu mʼdzikomo anakolola zochuluka.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zaka zisanu ndi ziwiri zakucuruka dzinthu nthaka inabala zambirimbiri.