Genesis 41:52 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adanenanso kuti, “Mulungu wandipatsa ana m'dziko la masautso anga.” Motero mwana wachiŵiriyo adamutcha Efuremu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo dzina la wachiwiri anamutcha Efuremu: chifukwa Mulungu anandibalitsa ine m'dziko la kusauka kwanga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wachiwiri wa mwamuna anamutcha Efereimu popeza anati, “Mulungu wandipatsa ana mʼdziko la masautso anga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo dzina la waciwiri anamucha Efraimu: cifukwa Mulungu anandibalitsa ine m'dziko la kusauka kwanga.