Genesis 41:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
kudafika zaka zisanu ndi ziŵiri za njala zimene ankanena Yosefe zija. Njala imeneyo inali itafikanso ku maiko ena onse, koma m'dziko lonse la Ejipito munali chakudya chambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo zinayamba kufika zaka zisanu ndi ziwiri za njala, monga ananena Yosefe; ndipo munali njala m'maiko monse; koma m'dziko lonse la Ejipito munali chakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo zaka zisanu ndi ziwiri za njala zija zinayamba monga ananenera Yosefe. Njalayi inafika ku mayiko ena onse koma ku dziko lonse la Igupto kunali chakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo zinayamba kufika zaka zisanu ndi ziwiri za njala, monga ananena Yosefe; ndipo munali njala m'maiko monse; koma m'dziko lonse la Aigupto munali cakudya.