Genesis 42:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe atamva kuti ku Ejipito ndiko kuli tirigu, adafunsa ana ake kuti, “Chifukwa chiyani mukungokhala osachitapo kanthu?
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anaona Yakobo kuti m'Ejipito munali tirigu, nati Yakobo kwa ana ake amuna, Chifukwa chanji mulinkuyang'anana?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo atamva kuti ku Igupto kuli tirigu, anati kwa ana ake, “Nʼchifukwa chiyani mukungoyangʼanana wina ndi mnzake?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anaona Yakobo kuti m'Aigupto munali tirigu, nati Yakobo kwa ana ace amuna, Cifukwa canji mulinkuyang'anana?