Genesis 42:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Iwo aja adayankha kuti, “Iyai mbuyathu, ife atumiki anu tabwera kuti tidzagule chakudya basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iwo anati kwa iye, Iai, mbuyanga, koma akapolo anu adzera kudzagula chakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anayankha, “Ayi mbuye wathu, antchito anufe tabwera kudzagula chakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iwo anati kwa iye, Iai, mbuyanga, koma akapolo anu adzera kudzagula cakudya.