Genesis 42:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yosefe adaŵayankha kuti, “Paja ndanena kale kuti ndinu azondi basi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yosefe anati kwa iwo, Ndicho chimene ndinakunenani inu, kuti, Ndinu ozonda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yosefe anawawuza kuti, “Ndi momwe ndaneneramo: Inu ndinu akazitape.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yosefe anati kwa iwo, dico cimene ndinakunenani inu, kuti, Ndinu ozonda.