Genesis 42:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono ndikuyesani motere; ndikulumbira kuti pali Farao! Inuyo simuchoka, mpaka mng'ono wanuyo atabwera kuno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mudzayesedwa ndi ichi, pali moyo wa Farao, simudzatuluka muno, koma akadze kuno mphwanu ndiko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndiye ndikuyesani motere: Ine ndikulumbira pali Farao ndithu, inuyo simudzachoka malo ano mpaka wotsirizayo atabwera kuno.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mudzayesedwa ndi ici, pali moyo wa Farao, simudzaturuka muno, koma akadze kuno mphwanu ndiko.