Genesis 42:18 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita masiku atatu, adaŵauza kuti, “Ine ndimaopa Mulungu. Choncho ndikupatsani mwai woupulumutsa moyo wanu mukachita izi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yosefe anati kwa iwo tsiku lachitatu, Chitani ichi, kuti mukhale ndi moyo; ine ndiopa Mulungu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku lachitatu Yosefe anawawuza kuti, “Popeza ine ndimaopa Mulungu, ndipo inuyo ngati mukufuna kukhala ndi moyo muchite izi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yosefe anati kwa iwo tsiku lacitatu, Citani ici, kuti mukhale ndi moyo; ine ndiopa Mulungu;