Genesis 42:23 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yosefe anali kumva zonse zimene ankakambiranazo, koma iwowo sadadziŵe, chifukwa choti ankalankhula naye kudzera mwa womasulira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo sanadziwe kuti Yosefe anamva; chifukwa anali ndi womasulira.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sanadziwe kuti Yosefe ankawamva popeza kuti ankagwiritsa ntchito wotanthauzira poyankhula naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo sanadziwa kuti, Yosefe anamva; cifukwa anali ndi womasulira.