Genesis 42:30 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Nduna yaikulu ya dzikolo idatilankhula mozaza, kuti ati ndife ozonda dziko laolo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kuti, Munthu mwini dziko, ananena ndi ife mwankhalwe, natiyesa ife ozonda dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Nduna yayikulu ya mʼdzikomo inatiyankhula mwa ukali kwambiri ndipo inkatiyesa kuti ndife akazitape.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kuti, Munthu mwini dziko, ananena ndi ife mwankharwe, natiyesa ife ozonda dziko.