Genesis 42:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife tidamuuza munthuyo kuti, ‘Ndife anthu okhulupirika, osati azondi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma ife tinati kwa iye, Tili anthu oona; sitili ozonda;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma tinamuwuza kuti, ‘Ndife anthu woona mtima osati akazitape.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma ife tinati kwa iye, Tiru anthu oona; sitiri ozonda;