Genesis 42:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife tonse tinalipo ana aamuna khumi ndi aŵiri, koma mmodzi adamwalira, ndipo wamng'ono ali ndi bambo wathu ku Kanani.’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
tili abale khumi ndi awiri, ana a atate wathu; wina palibe, ndipo lero wamng'ono ali ndi atate wathu m'dziko la Kanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ife tonse tinalipo ana aamuna khumi ndi awiri, abambo mmodzi. Mmodzi anamwalira, ndipo wamngʼono ali ndi abambo athu ku Kanaani.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
tiri abale khumi ndi awiri, ana a atate wathu; wina palibe, ndipo lero wamng'ono ali ndi atate wathu m'dziko la Kanani.