Genesis 42:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adakumbukira maloto aja onena za iwo, ndipo adati, “Ndinu anthu ozonda dziko. Mwabwera kuno kudzazonda kuti muwone ngati dziko lathu ndi lofooka.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yosefe anakumbukira maloto amene analota za iwo, ndipo anati kwa iwo, Ozonda inu; mwadzera kudzaona usiwa wa dziko.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo anakumbukira maloto aja amene analota za iwo ndipo anati, “Inu ndinu akazitape! Mwabwera kudzazonda dziko lathu kuti muone pamene palibe chitetezo.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yosefe anakumbukira maloto amene analoto za iwo, ndipo anati kwa iwo, Ozonda inu; mwadzera kudzaona usiwa wa dziko.