Genesis 43:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono banja la Yakobe lija litadya tirigu yense amene adaakasuma ku Ejipito uja, Yakobe adauza ana ake aja kuti, “Pitaninso, mukatigulireko chakudya pang'ono.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo panali pamene atatha kudya tirigu yense anatengayo ku Ejipito atate wao anati kwa iwo, Pitaninso, mukatigulire ife chakudya pang'ono.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono atatha kudya tirigu yense amene anakatenga ku Igupto, Yakobo anati kwa ana ake aja, “Pitani kuti mukatigulire chakudya china pangʼono.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo panali pamene atatha kudya tirigu yense anatengayo ku Aigupto atate wao anati kwa iwo, Pitaninso, mukatigulire ife cakudya pang'ono.