Genesis 43:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
namuuza kuti, “Pepani bwana, ife tidaabweranso kuno kale kudzagula chakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mfumu, tinatsikira ndithu nthawi yoyamba kudzagula chakudya:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Pepani mbuye wathu, ife tinabweranso ulendo woyamba kudzagula chakudya
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mfumu, tinatsikira ndithu nthawi yoyamba kudzagula cakudya: