Genesis 43:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono abalewo adakonzeratu mphatso zao zija kuti apereke kwa Yosefe masana, chifukwa anali atamva kuti akadya kumeneko.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakonzeratu mphatso asanafike Yosefe usana; chifukwa anamva kuti adzadya chakudya pamenepo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Abale aja anakonzeratu mphatso zawo zija kuti adzapereke kwa Yosefe, popeza anamva kuti Yosefe adzadya komweko masana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakonzeratu mphatso asanafike Yosefe usana; cifukwa anamva kuti adzadya cakudya pamenepo.