Genesis 43:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mukatilola kuti timtenge, tipita kukakugulirani chakudya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ngati mudzatuma mphwathu pamodzi ndi ife, tidzatsikira ndi kugulira inu chakudya.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mukalola kuti mngʼono wathuyu apite nafe, ndiye ife tidzapita kukakugulirani chakudya.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ngati mudzatuma mphwathu pamodzi ndi ife, tidzatsikira ndi kugulira inu cakudya.