Genesis 43:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ine ndikhale ngati chikole cha moyo wake wa Benjamini. Ngati sindidzabwerera naye kuno ali moyo, inu mudzandiimbe mlandu moyo wanga wonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ine ndidzakhala chikole, pa manja anga mudzamfunsa: ndikapanda kumbwezera kwa inu ndi kumuimitsa pamaso panu, chifukwa chake chidzakhala pa ine masiku onse:
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ine ndidzipereka kuti ndikhale chikole cha moyo wa mnyamatayu. Ine ndidzamuteteza. Ngati sindibwera naye ndi kumupereka kwa inu, ndidzakhala wolakwa pamaso panu moyo wanga wonse.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ine ndidzakhala cikole, pa manja anga mudzamfunsa: ndikapanda kumbwezera kwa inu ndi kumuimitsa pamaso panu, cifukwa cace cidzakhala pa ine masiku onse: