Genesis 44:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsopano mukanditengeranso uyu, nakaphedwa, ndiye kuti ine ndidzafa ndi chisoni.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ngati mukandichotsera ameneyonso, ndipo ngati chimgwera choipa, mudzanditsitsira ndi chisoni imvi zanga kumanda.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsopano mukanditengeranso uyu, nakaphedwa mu njira ndiye kuti mudzandikankhira ku manda ndi chisoni.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ngati mukandicotsera ameneyonso, ndipo ngati cimgwera coipa, mudzanditsitsira ndi cisoni imvi zanga kumanda.