Genesis 44:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwaberanji chikho chimene mbuyanga amamwera? Amati akafuna kudziŵa zam'tsogolo, amagwiritsa ntchito chikho chimenechi. Ndithu zimene mwachitazi nzoipa kwambiri.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi si ndicho chomwera nacho mbuyanga, naombeza ula nacho? Mwachitira choipa pakutero.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwaberanji chikho chimene mbuye wanga amamweramo ndi kugwiritsa ntchito akafuna kuwombeza? Chimene mwachitachi ndi chinthu choyipa.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi si ndico comwera naco mbuyanga, naombeza ula naco? Mwacitira coipa pakutero.