Genesis 45:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono nonsenu ndi Benjamini, mng'ono wangayu, mungathe kuwona kuti ndinedi amene ndikulankhula nanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Taonani, maso anu aona, ndi maso a mphwanga Benjamini, kuti ndi m'kamwa mwanga ndilikulankhula ndi inu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Tsono inu nonse pamodzi ndi mʼbale wangayu Benjamini, mukuona kuti ndi inedi amene ndikuyankhula nanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Taonani, maso anu aona, ndi maso a mphwanga Benjamini, kuti ndi m'kamwa mwanga ndirikulankhula ndi inu.