Genesis 45:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Farao adauza Yosefe kuti, “Uŵauze abale ako kuti asenzetse nyama zao katundu, ndipo abwerere ku Kanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Nena ndi abale ako, Chitani ichi; senzetsani nyama zanu, ndi kupita kunka ku dziko la Kanani;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Farao anati kwa Yosefe, “Uwawuze abale ako kuti, ‘Senzetsani nyama zanu katundu ndi kubwerera ku dziko la Kanaani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Nena ndi abale ako, Citani ici; senzetsani nyama zanu, ndi kupita kunka ku dziko la Kanani;