Genesis 45:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Asakade nkhaŵa kuti asiya katundu wao kumeneko, chifukwa dziko lokoma lachonde la ku Ejipito kuno lidzakhala lao.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musasamalire chuma chanu; popeza zabwino za dziko lonse la Ejipito ndi zanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Musadandaule zosiya katundu komweko chifukwa dziko lachonde la kuno ku Igupto lidzakhala lanu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musasamalire cuma canu; popeza zabwino za dziko lonse la Aigupto ndi zanu.