Genesis 45:25 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono iwo adachoka ku Ejipito, kubwerera ku Kanani kwa bambo wao Yakobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anakwera kutuluka m'Ejipito, nafika ku dziko la Kanani kwa Yakobo atate wao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo anachoka ku Igupto nafika kwa abambo awo Yakobo mʼdziko la Kanaani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anakwera kuturuka m'Aigupto, nafika ku dziko la Kanani kwa Yakobo atate wao.