Genesis 45:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adati, “Basi chabwino, mwana wanga Yosefe akali moyo. Ndipita ndikamuwone ndisanafe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo Israele anati, Chakwana; Yosefe mwana wanga akali ndi moyo; ndidzamuka ndikamuone iye ndisanafe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Israeli anati, “Ndatsimikizadi! Mwana wanga Yosefe akanali ndi moyodi. Ndipita ndikamuone ndisanafe.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo Israyeli anati, Cakwana; Yosefe mwana wanga akali ndi moyo; ndidzamuka ndikamuone iye ndisanafe.