Genesis 45:6 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chaka chino ndi chaka chachiŵiri cha njala. Koma zakhalabe zaka zisanu, ndipo pa zaka zimenezi anthu sadzalima kapena kukolola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Zaka ziwirizi muli njala m'dziko muno; ndipo zatsala zaka zisanu, zopanda kulima kapena kusenga.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kwa zaka ziwiri tsopano, kwakhala kuli njala mʼdziko muno, ndipo kwa zaka zisanu zikubwerazi, anthu sadzalima kapena kukolola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Zaka ziwirizi muli njala m'dziko muno; ndipo zatsala zaka zisanu, zopanda kulima kapena kusenga,