Genesis 45:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu adanditumiziratu ine kuno kuti ndikupulumutseni, kuti choncho ziwoneke zidzukulu zanu zambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mulungu anatumiza ine patsogolo panu kuti ndikhazike inu mutsale m'dziko lapansi, ndi kusunga inu amoyo ndi chipulumutso chachikulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mulungu ananditsogoza kuti adzakusungeni ndi moyo ndi kuti mudzakhale ndi zidzukulu pa dziko lapansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mulungu anatumiza ine patsogolo panu kuti ndikhazike inu mutsale m'dziko lapansi, ndi kusunga inu amoyo ndi cipulumutso cacikuru.