Genesis 46:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Simeoni anali aŵa: Yemuwele, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shaulo, amene mai wake anali mkazi wa ku Kanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana amuna a Simeoni: Yemuwele ndi Yamini, ndi Ohadi, ndi Yakini, ndi Zohari, ndi Shaulo, mwana wamwamuna wa mkazi wa ku Kanani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Simeoni ndi awa: Yemueli, Yamini, Ohadi, Yakini, Zohari ndi Shaulo amene mayi wake anali wa ku Kanaani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana amuna a Simeoni: Yemueli ndi Yamini, ndi Ohadi, ndi Yakini, ndi Zohari, ndi Sauli, mwana wamwamuna wa mkazi wa ku Kanani.