Genesis 46:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Yuda anali aŵa: Ere, Onani, Sela, Perezi ndi Zera, (koma Ere ndi Onani adaafera ku Kanani.) Ana a Perezi anali aŵa: Hezironi ndi Hamuli.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana amuna a Yuda: Eri, ndi Onani, ndi Sela, ndi Perezi, ndi Zera; koma Eri ndi Onani anafa m'dziko la Kanani. Ndi ana amuna a Perezi ndiwo Hezironi ndi Hamuli.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Yuda ndi awa: Eri, Onani, Sela, Perezi ndi Zera. Koma Eri ndi Onani anamwalira mʼdziko la Kanaani. Ana a Perezi anali Hezironi ndi Hamuli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana amuna a Yuda: Eri, ndi Onani, ndi Sela, ndi Perezi, ndi Zera; koma Eri ndi Onani anafa m'dziko la Kanani. Ndi ana amuna a Perezi ndiwo Hezroni ndi Hamuli.