Genesis 46:13 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Isakara anali aŵa: Tola, Puva, Iyobu ndi Simironi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana amuna a Isakara: Tola ndi Puva, ndi Iyobu, ndi Simironi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Isakara ndi awa: Tola, Puwa, Yobi ndi Simironi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana amuna a Isakara: Tola ndi Puva, ndi Yabi, ndi Simroni.