Genesis 46:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
(Ana ameneŵa ndiwo amene Leya adabalira Yakobe ku Mesopotamiya kuja, ndipo panalinso mwana wake wamkazi Dina. Adzukulu obadwa mwa Leya analipo 33 onse pamodzi.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amenewo ndi ana amuna a Leya, amene anambalira Yakobo m'Padanaramu, pamodzi ndi mwana wamkazi wake Dina; ana aamuna ndi aakazi onse ndiwo anthu makumi atatu kudza atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amenewa ndi ana aamuna a Leya amene anamubalira Yakobo ku Padanaramu. Panali mwana wamkazi dzina lake Dina. Ana onse analipo 33.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amenewo ndi ana amuna a Leya, amene anambalira Yakobo m'Padanaramu, pamodzi ndi mwana wamkazi wace Dina; ana amuna ndi akazi onse: ndiwo anthu makumi atatu kudza atatu.