Genesis 46:18 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
(Onseŵa anali adzukulu a Yakobe obadwa mwa Zilipa amene Labani adaapereka kwa mwana wake Leya.)
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wake wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amenewa ndi zidzukulu za Yakobo mwa Zilipa amene Labani anapereka kwa mwana wake, Leya. Onse pamodzi analipo 16.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Amenewa ndi ana a Zilipa, amene Labani anampatsa Leya mwana wace wamkazi, amenewo anambalira Yakobo, anthu khumi ndi asanu ndi mmodzi.