Genesis 46:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Rakele mkazi wa Yakobe anali aŵa: Yosefe ndi Benjamini.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ana a Rakele mkazi wake wa Yakobo: Yosefe ndi Benjamini.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana aamuna a Rakele mkazi wa Yakobo anali: Yosefe ndi Benjamini.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ana a Rakele mkazi wace wa Yakobo: Yosefe ndi Benjamini.