Genesis 46:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Manase ndi Efuremu anali ana amene Yosefe adabereka mwa Asenati, mwana wa Potifera wansembe wa ku Oni.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kwa Yosefe kunabadwa m'dziko la Ejipito Manase ndi Efuremu, amene Asenati mwana wamkazi wa Potifera wansembe wa Oni anambalira iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ku Igupto, Asenati mwana wa Potifara wansembe wa Oni, anamuberekera Yosefe ana awa: Manase ndi Efereimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kwa Yosefe kunabadwa m'dziko la Aigupto Manase ndi Efraimu, amene Asenati mwana wamkazi wa Potifera wansembe wa Oni anambalira iye.