Genesis 46:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dani anali ndi mwana mmodzi yekha dzina lake Husimu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi ana amuna a Dani: Husimu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwana wa mwamuna wa Dani anali: Husimu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi ana amuna a Dani: Husimu.