Genesis 46:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Yosefe adauza abale ake aja pamodzi ndi banja lonse la bambo wake kuti “Ndipita ndikamuuze Farao kuti abale anga pamodzi ndi onse a m'banja la atate anga amene ankakhala ku Kanani, abwera kuno kwa ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yosefe anati kwa abale ake, ndi kwa mbumba ya atate wake, Ndidzanka, ndikauze Farao, ndipo ndidzati kwa iye, Abale anga ndi mbumba ya atate wanga, amene anali m'dziko la Kanani, afika kwa ine;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo Yosefe anati kwa abale ake pamodzi ndi a pa banja la abambo ake, “Ndipita kwa Farao ndipo ndikamuwuza kuti, ‘Abale anga pamodzi ndi onse a mʼnyumba ya abambo anga amene amakhala mʼdziko la Kanaani abwera kuno kwa ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yosefe anati kwa abale ace, ndi kwa mbumba ya atate wace, Ndidzanka, ndikauze Farao, ndipo ndidzati kwa iye, Abale anga ndi mbumba ya atate wanga, amene anali m'dziko la Kanani, afika kwa ine;