Genesis 46:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Anthu ameneŵa ndi abusa, amaŵeta zoŵeta. Nkhosa zao ndi ng'ombe zomwe abwera nazo, pamodzi ndi zinthu zao zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo anthuwo ali abusa chifukwa anakhala oweta ng'ombe; ndipo anadza ndi nkhosa zao ndi ng'ombe zao ndi zonse ali nazo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anthuwa ndi abusa; amaweta ziweto zawo ndipo abwera ndi nkhosa ndi ngʼombe zawo, pamodzi ndi antchito awo.’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo anthuwo ali abusa cifukwa anakhala oweta ng'ombe; ndipo anadza ndi nkhosa zao ndi ng'ombe zao ndi zonse ali nazo.