Genesis 46:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Farao akakuitanani, ndipo akakufunsani kuti, ‘Mumagwira ntchito yanji?’
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo padzakhala pamene Farao adzaitana inu, nadzati, Ntchito yanu njotani?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono Farao akakuyitanani nakufunsani kuti, ‘Kodi mumagwira ntchito yanji?’
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo padzakhala pamene Farao adzaitana inu, nadzati, Nchito yanu njotani?