Genesis 46:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adatenga zoŵeta zao zonse pamodzi ndi zinthu zonse zimene anali nazo ku Kanani, ndipo adapita ku Ejipito. Yakobe adatenga zidzukulu zake zonse,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anatenga ng'ombe zao ndi chuma chao anachipeza m'dziko la Kanani, nadza ku Ejipito, Yakobo ndi mbeu zake zonse pamodzi ndi iye;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iwo anatenganso ziweto zawo ndi katundu wawo amene anali naye ku Kanaani, ndipo Yakobo pamodzi ndi ana ndi zidzukulu zake anapita ku Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anatenga ng'ombe zao ndi cuma cao anacipezam'dziko la Kanani, nadza ku Aigupto, Yakobo ndi mbeu zace zonse pamodzi ndi iye;