Genesis 46:8 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Naŵa maina a Aisraele amene adapita ku Ejipito, ndiye kuti Yakobe ndi ana ake. Rubeni, mwana wachisamba wa Yakobe,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Maina a ana a Israele amene anadza m'Ejipito ndi awa: Yakobo ndi ana amuna ake: Rubeni mwana wamwamuna woyamba wa Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nawa ana a Israeli (ndiye kuti Yakobo ndi ana ake) amene anapita ku Igupto: Rubeni mwana woyamba wa Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Maina a ana a Israyeli amene anadza m'Aigupto ndi awa: Yakobo ndi ana amuna ace: Rubeni mwana wamwamuna woyamba wa Yakobo.