Genesis 47:21 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yosefe adaŵasandutsa akapolo anthuwo ponseponse m'dziko la Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono anthu, anasunthira iwo kumidzi kuchokera kumphepete kwa malire a Ejipito kufikira kumphepete kwina kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
ndipo Yosefe anawasandutsa anthu onse kukhala akapolo a Farao, kuchokera ku malire a mbali ina ya Igupto kukafika ku malire a mbali ina ya dzikolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono anthu, anasunthira iwo ku midzi kucokera kumphepete kwa malire a Aigupto kufikira kumphepete kwina kwace.