Genesis 47:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adakhala ku Ejipito, zaka 17, choncho zaka za moyo wake zidakwanira 147.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anakhala m'dziko la Ejipito zaka khumi mphambu zisanu ndi ziwiri; ndipo masiku a Yakobo zaka za moyo wake zinali zaka zana limodzi mphambu makumi anai kudza zisanu ndi ziwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anakhala ku Igupto zaka 17 ndipo zaka za moyo wake zinali 147.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anakhala m'dziko la Aigupto zaka khumi mphambu zisanu ndi ziwiri; ndipo masiku a Yakobo zaka za moyo wace zinali zaka zana limodzi mphambu makumi anai kudza zisanu ndi ziwiri.