Genesis 47:3 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Farao adaŵafunsa kuti, “Kodi mumagwira ntchito yanji?” Iwo adayankha kuti, “Ndife abusa bwana, monga momwe ankachitira makolo athu.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Farao anati kwa abale ake, Ntchito yanu njotani? Ndipo iwo anati kwa Farao, Akapolo anu ndi abusa, ife ndi atate athu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Farao anafunsa abale akewo kuti, “Mumagwira ntchito yanji?” Iwo anamuyankha kuti, “Ife, bwana ndife oweta ziweto, monga ankachitira makolo athu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Farao anati kwa abale ace, Nchito yanu njotani? ndipo iwo anati kwa Farao, Akapolo anu ndi abusa, ife ndi atate athu.