Genesis 49:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake Yakobe adaitana ana ake naŵauza kuti, “Sonkhanani pamodzi, kuti ndikuuzeni zimene zidzakuchitikireni m'tsogolo muno.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anaitana ana ake amuna, nati, Sonkhanani inu, kuti ndikuuzeni inu chimene chidzakugwerani inu masiku akudzawo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pambuyo pake Yakobo anayitanitsa ana ake aamuna nati: Sonkhanani pamodzi kuti ndikuwuzeni zimene zidzakuchitikireni mʼmasiku a mʼtsogolo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anaitana ana ace amuna, nati, Sonkhanani inu, kuti ndikuuzeni inu cimene cidzakugwerani inu masiku akudzawo.