Genesis 49:10 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndodo yaufumu siidzachoka mwa Yuda, adzachita kuupanira ufumu umenewo, adzasunga mphamvu zake, mpaka mwiniwake weniweni atabwera, wodzalamulira anthu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndodo yachifumu siidzachoka mwa Yuda, kapena wolamulira pakati pa mapazi ake, kufikira atadza Silo; ndipo anthu adzamvera iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndodo yaufumu sidzachoka mwa Yuda, udzawupanirira ulamuliro motero kuti palibe amene adzawuchotse, mpaka mwini wake weniweni atabwera ndipo mitundu yonse ya anthu idzamumvera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndodo yacifumu siidzacoka mwa Yuda, Kapena wolamulira pakati pa mapazi ace, Kufikira atadza Silo; Ndipo anthu adzamvera iye.