Genesis 49:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Isakara ali ngati bulu wamphamvu, amagona chotambasuka pakati pa makola.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Isakara ndiye bulu wolimba, alinkugona pakati pa makola.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Isakara ali ngati bulu wamphamvu wogona pansi pakati pa makola.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Isakara ndiye buru wolimba, Alinkugona pakati pa makola;