Genesis 49:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Gadi anthu achifwamba adzamthira nkhondo, koma iyeyo adzaŵatembenukira nkuŵapirikitsa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndi Gadi, achifwamba adzampsinja iye; koma iye adzapsinja pa chitende chao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Gadi adzachitidwa chiwembu ndi gulu la amaliwongo, koma iye adzawathamangitsa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndi Gadi, acifwamba adzampsinja iye; Koma iye adzapsinja pa citende cao.